2 Mafumu 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zedekiya ankachita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene Yehoyakimu anachita.+