2 Mafumu 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu komanso akuluakulu a magulu a asilikali, anathawira ku Iguputo,+ chifukwa ankaopa Akasidi.+
26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu komanso akuluakulu a magulu a asilikali, anathawira ku Iguputo,+ chifukwa ankaopa Akasidi.+