-
2 Mafumu 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anthuwo anayankha kuti: “Munthu wina anabwera kudzakumana nafe nʼkutiuza kuti, ‘Bwererani kwa mfumu imene yakutumani ndipo mukaiuze kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu kuti utumize anthu kukafunsa kwa Baala-zebabu mulungu wa ku Ekironi? Choncho pabedi pamene wagonapo, sudzukapo, chifukwa ndithu umwalira.’”’”+
-