-
2 Mafumu 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako mfumuyo inatumizanso mtsogoleri wina wa asilikali 50 pamodzi ndi asilikali ake 50. Mtsogoleriyo anauza Eliya kuti: “Munthu wa Mulungu woona iwe! Mfumu ikuti, ‘Utsike pamenepo msanga!’”
-