-
2 Mafumu 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Koma Eliya anawayankha kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu woona, moto uchokere kumwamba ndipo upsereze iweyo ndi asilikali ako 50.” Moto wa Mulungu unabweradi kuchokera kumwamba nʼkupsereza mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.
-