-
2 Mafumu 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno mfumuyo inatumizanso mtsogoleri wachitatu wa asilikali 50 pamodzi ndi asilikali ake 50. Koma mtsogoleri ameneyo atafika, anagwada nʼkuyamba kuchonderera Eliya kuti awachitire chifundo. Iye anati: “Inu munthu wa Mulungu woona, chonde muone moyo wanga ndiponso wa atumiki anu 50 awa kukhala wamtengo wapatali.
-