-
2 Mafumu 2:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno Eliya anauza Elisa kuti: “Iweyo utsale kuno, chifukwa Yehova wandituma ku Yorodano.” Koma Elisa anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.” Choncho iwo anapitiriza ulendo wawo.
-