-
2 Mafumu 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno ana a aneneri okwana 50 anaima chapatali nʼkumawayangʼana. Koma Eliya ndi Elisa anaima pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.
-