-
2 Mafumu 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Eliya anati: “Wapempha chinthu chovuta. Ukandiona ndikutengedwa, zimene wapemphazi zikuchitikiradi, koma ukapanda kundiona, sizichitika.”
-