-
2 Mafumu 2:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma iwo anamʼkakamiza mpaka iye anachita manyazi, moti anati: “Atumeni.” Choncho anatuma amuna 50 ndipo anamufufuza kwa masiku atatu koma sanamʼpeze.
-