2 Mafumu 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthuwo atabwerera kwa Elisa ku Yeriko,+ Elisa ananena kuti: “Pajatu ndinakuuzani kuti musapite.”