2 Mafumu 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Patapita nthawi, anthu amumzindawo anauza Elisa kuti: “Inu mbuyathu mukudziwa kuti mzindawu uli pamalo abwino,+ koma madzi ake ndi oipa ndipo nthaka ndi yosabereka.”*
19 Patapita nthawi, anthu amumzindawo anauza Elisa kuti: “Inu mbuyathu mukudziwa kuti mzindawu uli pamalo abwino,+ koma madzi ake ndi oipa ndipo nthaka ndi yosabereka.”*