-
2 Mafumu 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Komanso anatumiza uthenga kwa Yehosafati mfumu ya Yuda wakuti: “Mfumu ya Mowabu yandigalukira. Kodi tipita limodzi kukamenya nkhondo ku Mowabu?” Yehosafati anayankha kuti: “Inde ndipita.+ Inu ndi ine ndife amodzi. Anthu anu ndi anthu anga ndi amodzi. Mahatchi anga nʼchimodzimodzi ndi mahatchi anu.”+
-