2 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako mfumu ya Isiraeli inanyamuka limodzi ndi mfumu ya Yuda komanso mfumu ya Edomu.+ Atayenda mozungulira kwa masiku 7, mʼchipululumo munalibe madzi oti anthuwo amwe pamodzi ndi ziweto zimene ankayenda nazo.
9 Kenako mfumu ya Isiraeli inanyamuka limodzi ndi mfumu ya Yuda komanso mfumu ya Edomu.+ Atayenda mozungulira kwa masiku 7, mʼchipululumo munalibe madzi oti anthuwo amwe pamodzi ndi ziweto zimene ankayenda nazo.