2 Mafumu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho mukagwetse mzinda uliwonse wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ komanso mzinda uliwonse wabwino kwambiri ndipo mukadule mtengo uliwonse wabwino. Mukatseke akasupe onse amadzi nʼkuwononga malo alionse abwino poponyapo miyala.”+
19 Choncho mukagwetse mzinda uliwonse wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ komanso mzinda uliwonse wabwino kwambiri ndipo mukadule mtengo uliwonse wabwino. Mukatseke akasupe onse amadzi nʼkuwononga malo alionse abwino poponyapo miyala.”+