2 Mafumu 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno pa nthawi yopereka nsembe yambewu mʼmawa,+ anangoona madzi akuchokera cha ku Edomu ndipo malo onsewo anadzaza madzi.
20 Ndiyeno pa nthawi yopereka nsembe yambewu mʼmawa,+ anangoona madzi akuchokera cha ku Edomu ndipo malo onsewo anadzaza madzi.