2 Mafumu 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ataona zimenezi ananena kuti: “Amenewa ndi magazi. Ndiye kuti mafumu aja aphana okhaokha ndi lupanga. Amowabu inu, tiyeni tikatenge zinthu zawo!”+
23 Ataona zimenezi ananena kuti: “Amenewa ndi magazi. Ndiye kuti mafumu aja aphana okhaokha ndi lupanga. Amowabu inu, tiyeni tikatenge zinthu zawo!”+