2 Mafumu 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo atalowa mumsasa wa Aisiraeli, Aisiraeli anayamba kuwapha. Amowabuwo anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa nʼkumawapha mpaka kukafika ku Mowabu.
24 Iwo atalowa mumsasa wa Aisiraeli, Aisiraeli anayamba kuwapha. Amowabuwo anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa nʼkumawapha mpaka kukafika ku Mowabu.