2 Mafumu 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atamuuza zimenezi, mayiyo ananyamuka. Iye ndi ana ake atadzitsekera mʼnyumba, anawo ankamuikira zotengera zija pafupi, iye nʼkumathiramo mafuta.+
5 Atamuuza zimenezi, mayiyo ananyamuka. Iye ndi ana ake atadzitsekera mʼnyumba, anawo ankamuikira zotengera zija pafupi, iye nʼkumathiramo mafuta.+