-
2 Mafumu 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako anapita kwa munthu wa Mulungu woona uja kukamuuza zomwe zinachitikazo. Munthu wa Mulungu woonayo anati: “Pita ukagulitse mafutawo nʼkubweza ngongole zako ndipo ndalama zotsalazo zikuthandize iweyo ndi ana ako.”
-