-
2 Mafumu 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Komabe, mayiyo anakhala ndi pakati nthawi ngati yomweyo chaka chotsatira ndipo anabereka mwana wamwamuna mogwirizana ndi zimene Elisa anamuuza.
-