-
2 Mafumu 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kumeneko mwanayo anayamba kulira kuti: “Mutu wanga ine! Mayo ine mutu wanga!” Kenako bambo akewo anauza wantchito wawo wina kuti: “Munyamule upite naye kwa mayi ake.”
-