2 Mafumu 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wantchitoyo ananyamuladi mwanayo nʼkupita naye kwa mayi ake. Mayi akewo anamunyamula pamwendo mpaka masana, kenako mwanayo anamwalira.+
20 Wantchitoyo ananyamuladi mwanayo nʼkupita naye kwa mayi ake. Mayi akewo anamunyamula pamwendo mpaka masana, kenako mwanayo anamwalira.+