-
2 Mafumu 4:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako anaitana mwamuna wake nʼkumuuza kuti: “Mundipatseko wantchito mmodzi ndi bulu mmodzi. Ndikufuna ndipite mwamsanga kwa munthu wa Mulungu woona uja.”
-