2 Mafumu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwamuna wakeyo anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukufuna kupitako lero? Lerotu si tsiku limene mwezi watsopano uoneke+ komanso si la sabata.” Koma mayiyo anayankha kuti: “Zonse zili bwino.”
23 Mwamuna wakeyo anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukufuna kupitako lero? Lerotu si tsiku limene mwezi watsopano uoneke+ komanso si la sabata.” Koma mayiyo anayankha kuti: “Zonse zili bwino.”