2 Mafumu 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Gehazi anatsogola ndipo anakaika ndodo ija pankhope ya mwanayo, koma sipanamveke mawu kapena chizindikiro chosonyeza kuti ali moyo.+ Choncho iye anabwerera nʼkukauza Elisa kuti: “Mwana uja sanadzuke.”
31 Gehazi anatsogola ndipo anakaika ndodo ija pankhope ya mwanayo, koma sipanamveke mawu kapena chizindikiro chosonyeza kuti ali moyo.+ Choncho iye anabwerera nʼkukauza Elisa kuti: “Mwana uja sanadzuke.”