2 Mafumu 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno analowa kuchipinda nʼkutseka chitseko ndipo analiko awiriwiri. Atatero anayamba kupemphera kwa Yehova.+
33 Ndiyeno analowa kuchipinda nʼkutseka chitseko ndipo analiko awiriwiri. Atatero anayamba kupemphera kwa Yehova.+