2 Mafumu 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno Elisa anaitana Gehazi nʼkumuuza kuti: “Pita ukaitane mayi a mwanayu.”* Gehazi anaitana mayiyo ndipo anabweradi. Elisa anauza mayiyo kuti: “Dzamutengeni mwana wanu.”+
36 Ndiyeno Elisa anaitana Gehazi nʼkumuuza kuti: “Pita ukaitane mayi a mwanayu.”* Gehazi anaitana mayiyo ndipo anabweradi. Elisa anauza mayiyo kuti: “Dzamutengeni mwana wanu.”+