-
2 Mafumu 4:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Kenako anapatsa ana a aneneriwo chakudyacho kuti adye. Koma atangoyamba kudya, anakuwa kuti: “Inu munthu wa Mulungu woona, mumphikamu muli poizoni!” Ndipo sanathenso kudya.
-