2 Mafumu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kamtsikanako kanauza mbuye wake wamkazi kuti: “Abwanawa akanapita kwa mneneri+ amene ali ku Samariya, bwenzi atakawachiritsa khate lawo.”+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, ptsa. 9-108/1/2005, tsa. 10
3 Kamtsikanako kanauza mbuye wake wamkazi kuti: “Abwanawa akanapita kwa mneneri+ amene ali ku Samariya, bwenzi atakawachiritsa khate lawo.”+