2 Mafumu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu ya Siriya inauza Namani kuti: “Nyamuka upite. Nditumiza kalata kwa mfumu ya Isiraeli.” Choncho iye ananyamuka atatenga matalente* 10 a siliva, masekeli* 6,000 a golide ndi zovala 10.
5 Ndiyeno mfumu ya Siriya inauza Namani kuti: “Nyamuka upite. Nditumiza kalata kwa mfumu ya Isiraeli.” Choncho iye ananyamuka atatenga matalente* 10 a siliva, masekeli* 6,000 a golide ndi zovala 10.