-
2 Mafumu 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Namani anapititsa kalatayo kwa mfumu ya Isiraeli. Mʼkalatayo analembamo kuti: “Ndatumiza kalatayi komanso mtumiki wanga Namani kuti mumʼchiritse khate lake.”
-