-
2 Mafumu 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Namani atamva zimenezi anapsa mtima ndipo ananyamuka nʼkumapita. Iye anati: “Ine ndimaganiza kuti abwera kudzaima nane pafupi nʼkuitana dzina la Yehova Mulungu wake, kwinaku akuyendetsa dzanja lake uku ndi uku pamwamba pa khateli kuti andichiritse.
-