2 Mafumu 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi Abana ndi Faripara, mitsinje ya ku Damasiko,+ si yabwino kuposa madzi onse a mu Isiraeli? Sindingathe kukasamba mmenemo nʼkuyeretsedwa?” Atatero anatembenuka nʼkumapita atakwiya kwambiri.
12 Kodi Abana ndi Faripara, mitsinje ya ku Damasiko,+ si yabwino kuposa madzi onse a mu Isiraeli? Sindingathe kukasamba mmenemo nʼkuyeretsedwa?” Atatero anatembenuka nʼkumapita atakwiya kwambiri.