-
2 Mafumu 5:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Gehazi anathamangiradi Namani ndipo Namani ataona kuti munthu akumʼthamangira, anatsika pagaleta lake kuti akumane naye. Kenako anati: “Nʼkwabwino?”
-