2 Mafumu 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Gehazi anayankha kuti: “Inde nʼkwabwino. Mbuyanga wandituma kuti, ‘Posachedwapa kwabwera anyamata awiri, ana a aneneri, kuchokera kudera lamapiri la Efuraimu. Muwapatseko talente imodzi ya siliva ndi zovala ziwiri.’”+
22 Gehazi anayankha kuti: “Inde nʼkwabwino. Mbuyanga wandituma kuti, ‘Posachedwapa kwabwera anyamata awiri, ana a aneneri, kuchokera kudera lamapiri la Efuraimu. Muwapatseko talente imodzi ya siliva ndi zovala ziwiri.’”+