2 Mafumu 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Namani anamuuza kuti: “Chabwino. Tenga matalente awiri.” Anamuumiriza+ ndipo anamʼmangira matalente awiri a siliva mʼmatumba awiri ndi zovala ziwiri. Anapereka zinthuzo kwa atumiki ake awiri kuti amunyamulire.
23 Namani anamuuza kuti: “Chabwino. Tenga matalente awiri.” Anamuumiriza+ ndipo anamʼmangira matalente awiri a siliva mʼmatumba awiri ndi zovala ziwiri. Anapereka zinthuzo kwa atumiki ake awiri kuti amunyamulire.