2 Mafumu 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atafika ku Ofeli,* Gehazi anawalandira anthuwo katunduyo ndipo anamuika mʼnyumba nʼkuwauza kuti azipita. Anthuwo atapita,
24 Atafika ku Ofeli,* Gehazi anawalandira anthuwo katunduyo ndipo anamuika mʼnyumba nʼkuwauza kuti azipita. Anthuwo atapita,