2 Mafumu 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gehazi anapita kukaima pafupi ndi mbuye wake. Kenako Elisa anamʼfunsa kuti: “Kodi unapita kuti Gehazi?” Koma iye anayankha kuti: “Ine mtumiki wanu sindinapite kulikonse.”+
25 Gehazi anapita kukaima pafupi ndi mbuye wake. Kenako Elisa anamʼfunsa kuti: “Kodi unapita kuti Gehazi?” Koma iye anayankha kuti: “Ine mtumiki wanu sindinapite kulikonse.”+