26 Ndiyeno Elisa anati: “Kodi mtima wanga sunali nawe limodzi pamene munthuyo amatsika pagaleta lake kuti akumane nawe? Kodi ino ndi nthawi yolandira siliva, zovala, minda ya maolivi, minda ya mpesa, nkhosa, ngʼombe, antchito aamuna kapena antchito aakazi?+