2 Mafumu 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano khate la Namani+ libwera kwa iweyo ndi mbadwa zako ndipo silidzachoka mpaka kalekale.” Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate moti anayera kwambiri.+
27 Tsopano khate la Namani+ libwera kwa iweyo ndi mbadwa zako ndipo silidzachoka mpaka kalekale.” Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate moti anayera kwambiri.+