2 Mafumu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfumu ya Isiraeli inatumiza uthenga wochenjeza anthu akumalo amene munthu wa Mulungu woona uja ananena. Elisa anachenjeza mfumu ya Isiraeli maulendo angapo* ndipo akaichenjeza sinkapitako.+
10 Mfumu ya Isiraeli inatumiza uthenga wochenjeza anthu akumalo amene munthu wa Mulungu woona uja ananena. Elisa anachenjeza mfumu ya Isiraeli maulendo angapo* ndipo akaichenjeza sinkapitako.+