-
2 Mafumu 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Zimenezi zinakwiyitsa kwambiri mfumu ya Siriya, choncho inaitanitsa atumiki ake nʼkuwafunsa kuti: “Ndiuzeni, ndi ndani pa gulu lathuli amene ali kumbali ya mfumu ya Isiraeli?”
-