2 Mafumu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho mfumuyo inati: “Pitani mukafufuze kumene ali kuti nditumizeko anthu akamugwire.” Kenako mfumuyo inauzidwa kuti: “Ali ku Dotani.”+
13 Choncho mfumuyo inati: “Pitani mukafufuze kumene ali kuti nditumizeko anthu akamugwire.” Kenako mfumuyo inauzidwa kuti: “Ali ku Dotani.”+