2 Mafumu 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Asiriyawo atayamba kupita kumene kunali Elisa, iye anapemphera kwa Yehova kuti: “Chonde chititsani khungu+ mtundu uwu.” Choncho Mulungu anawachititsa khungu mogwirizana ndi zimene Elisa anapempha.
18 Asiriyawo atayamba kupita kumene kunali Elisa, iye anapemphera kwa Yehova kuti: “Chonde chititsani khungu+ mtundu uwu.” Choncho Mulungu anawachititsa khungu mogwirizana ndi zimene Elisa anapempha.