2 Mafumu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Elisa anawauza kuti: “Njira yake si imeneyi ndipo mzinda wake si umenewu. Nditsatireni, ndikulondolerani kwa munthu amene mukufuna.” Koma anawapititsa ku Samariya.+
19 Kenako Elisa anawauza kuti: “Njira yake si imeneyi ndipo mzinda wake si umenewu. Nditsatireni, ndikulondolerani kwa munthu amene mukufuna.” Koma anawapititsa ku Samariya.+