2 Mafumu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma msilikali wothandiza mfumu amene mfumu inkamudalira, anayankha munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba, kodi zimenezo zingachitike?”+ Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako,+ koma sudya nawo.”+
2 Koma msilikali wothandiza mfumu amene mfumu inkamudalira, anayankha munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba, kodi zimenezo zingachitike?”+ Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako,+ koma sudya nawo.”+