-
2 Mafumu 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho ananyamuka kukungoyamba kumene kuda, kupita kumsasa wa Asiriya. Koma atafika mʼmbali mwa msasawo, anapeza kuti munalibe aliyense.
-