-
2 Mafumu 7:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Akhate aja atafika mʼmbali mwa msasawo, analowa mutenti ina ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Kenako anatengamo siliva, golide ndi zovala nʼkupita kukazibisa. Atatero anabwerera nʼkudzalowanso mutenti ina ndipo anatengamonso zinthu zina nʼkukazibisa.
-