-
2 Mafumu 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako anayamba kuuzana kuti: “Zimene tikuchitazi si zabwino. Tiyeni tikauze ena nkhani yabwinoyi! Tikazengereza mpaka kucha, tikhala ndi mlandu woyenera kulangidwa. Tiyeni tipite tikanene nkhaniyi kunyumba ya mfumu.”
-